Makina owerengera
Kukula kwa contract = -
Kukula kwa pip = -
Leverage Yeniyeni = -
Kukula kwa point = -
Zotsatira
Margin Yofunika
$
Momwe mungawerengere zosowa za margin
Margin yofunika = Kuchuluka ÷ Effective leverage* * Gwiritsani ntchito denominator ya chiŵerengero cha Effective leverage, 1 : XXXX. Kuchuluka kumawerengedwa potengera fomula iyi:
Fomula
Margin yofunika = Kuchuluka ÷ Effective leverage*
* Gwiritsani ntchito denominator ya chiŵerengero cha Effective leverage, 1 : XXXX.
Kuchuluka kumawerengedwa potengera fomula iyi:
- Forex: Lots x Kukula kwa contract x BSE/USD*
- Zina: Lots x Kukula kwa contract x Mtengo wogulitsira x QTE/USD**
*BSE/USD ndi mtengo wosinthanitsa kuchokera ku ndalama yoyambira (BSE), yotchedwa "Margin Currency" mu MT5, kupita ku USD.
**QTE/USD ndi mtengo wosinthanitsa kuchokera ku ndalama yotchulidwa (QTE), yotchedwa "Profit Currency" mu MT5, kupita ku USD.
Chitsanzo
Mukumalonda ma lots 0.25 a EUR/GBP ndi leverage ya 1:1000. Mtengo wosinthanitsa EUR kupita ku USD ndi 1.10634.
Margin yofunika ndi USD 27.66 kutsegula positon yomwe tafotokozayi.
Chidziwitso: Awa ndi mitengo yoyerekeza okha ndipo adzasiyana kutengera leverage yomwe yakhazikitsidwa pa akaunti yanu ndi chuma chomwe mukufuna kuchichita malonda.

Momwe mungagwiritse ntchito makina owerengera margin a Deriv
Sankhani chida chamalonda
Sankhani chida chanu chamalonda, kuchokera ku Forex, Masheya, Commodities, Crypto, ndi zina.
Lowetsani kukula kwa position
Lowetsani kuchuluka kwa malonda anu mu lots. Mungathenso kusintha mtengo wa chuma kuti mugwirizanitse kuwerengera ndi njira yanu yamalonda.
Onani zosowa za margin
Onani margin yeniyeni yofunikira pa chida chamalonda chomwe mwasankha.
N'chifukwa chiyani mugwiritse ntchito makina owerengera margin a Deriv
Makina owerengera margin a Deriv amakuthandizani kudziwa margin yomwe malonda aliwonse amafunikira ndikukonzekera positions zina popanda kuika akaunti yanu pachiwopsezo chochuluka.
Pewani chiwopsezo cha margin call
Onani margin yofunika musanatsegule malonda kuti muchepetse chiwopsezo cha kutsekedwa kwa positions kokha.

Yang'anirani kukula kwa malonda anu
Werengani kukula kwa position koyenera kogwirizana ndi ndalama zanu zomwe muli nazo ndi momwe mungapirire chiwopsezo.

Sinthani positions zambiri
Onani margin yomwe malonda aliwonse amagwiritsa ntchito kuti mukonzekere positions zina.

Makina owerengera ogwirizana
Makina owerengera pip
Sinthani manambala a pip kukhala ndalama za dollar pa malonda anu. Werengani molondola kuchuluka kwa phindu kapena kutaika komwe kusintha kulikonse kwa mtengo kumatanthauza.
Makina owerengera swap
Onani zomwe kusunga positions usiku wonse kudzawononga kapena kupeza. Werengani ndalama za tsiku ndi tsiku kuti musankhe ngati malonda otalikirapo agwirizana ndi njira yanu.