Chifukwa chiyani muyenera kuchita malonda a Synthetic Indices ndi Deriv
Malonda a 24/7
Mupeza Synthetic Indices nthawi zonse, kuphatikizapo Loweruka, Lamlungu ndi maholide.

Zopanda chikoka cha zochitika zapadziko lapansi
Misika yopangidwa (simulated) yomwe siikhudzidwa ndi maola wamba a msika kapena chiwopsezo cha msika weniweni ndi liquidity.

Leverage mpaka 1:1000
Gwiritsani ntchito Leverage mpaka 1:1000 pazinthu zina kuti mupindule bwino ndi ndalama zanu.

Zomwe timapereka
Crash/Boom Indices
Sankhani pakati pa Crash Indices pa kutsika kwadzidzidzi kapena Boom Indices pa kukwera kwachangu. Sinthani kuchuluka kwa tick kukhala 50, 150, 300, 500, 600, 900, kapena 1,000 kuti muwone kathyathyathya ka nthawi imene msika wanu udzagwa kapena kukwera.
Volatility Indices
Sankhani pakati pa mitundu yosiyanasiyana ya volatility yokhazikika kuyambira 10% yofatsa mpaka 250% yamphamvu. Komanso, sinthani liwiro la tick kukhala kamodzi pamasekondi 2 pa kuthamanga kwa nthawi zonse, kapena pasekondi imodzi pa zochitika zachangu.
Hybrid Indices
Onani mmene Crash/Boom indices zimaonekera modziwikiratu ndi kuwonjezeka kwa volatility kwa 20%. Pezani masinthidwe ozikidwa pa misika yeniyeni, kuphatikiza njira zokhazikika ndi masinthidwe adzidzidzi.
Volatility Switch Indices
Chitani malonda pansi pa mikhalidwe yosinthasintha ya msika pogwiritsa ntchito milingo ya volatility monga 10%, 50%, kapena 100%, iliyonse imakhalapo pakati pa mphindi 5 mpaka 60 pafupifupi.
Step Indices
Pa tick iliyonse, mtengo wa chinthu ichi umakwera kapena kutsika ndi 0.1, 0.2, 0.3, 0.4, kapena 0.5 — popanda kusintha kwadzidzidzi kapena njira zovuta. Ndi kusintha kokhazikika, mosatsatira.
Drift Switching Indices
Zinthu izi zimasinthasintha pakati pa njira za bullish, bearish, kapena sidewaylon. Zabwino kwambiri pa kugula kwanzeru, kugulitsa kwaluso, ndi kuyima panthawi yoyenera. Ndipo chokoma kwambiri? Kusinthaku kumatenga pafupifupi mphindi 10, 20, kapena 30, kotero mutha kukonzekera patsogolo.
Trek Indices
Masinthidwe ambiri a mtengo ndi ang'onoang'ono, koma kugawidwa kumakhalabe ndi masinthidwe akuluakulu mbali imodzi. Sankhani kukwera kapena kutsika kuti mulowe m'misika ya volatility ya 30% ya mbali yomwe mwasankha.
Skew Step Indices
Pitirizani kupitirira Step Indices zanthawi zonse ndi kuchita malonda ndi kukula kosiyanasiyana kwa masitepe komanso mwayi wosiyanasiyana. Ndi mwayi wa 80% kapena 90% pa kusintha kaang'ono komanso 10% kapena 20% pa kusintha kwakukulu, tick iliyonse imapereka mwayi wopindula ndi kusintha kwamsika.
DEX Indices
Dikirani kukwera ndi kutsika kwakukulu pakati pa mphindi 10, 15, kapena 25 (pafupifupi) ndi kusintha kwakung'ono pakati pake.
Jump Indices
Dikirani mitengo kudumpha pakati pa mphindi 20 (pafupifupi), ndi mwayi wofanana wokwera kapena kutsika pafupifupi nthawi 30 kuposa volatility wamba wa index. Mutha kusankha pakati pa 10%, 25%, 50%, 75%, ndi 100% volatility.
Daily Reset Indices
Zinthu izi zimatsanzira zochitika zosavuta za bull (kukwera) ndi bear (kutsika) pamsika. Zimasonyeza kukwera kwa chuma chenicheni chomwe chimayendetsedwa ndi malingaliro abwino kapena kutsika kochokera ku malingaliro oipa. Index iliyonse imabwerera ku muyeso woyambira tsiku lililonse.
Range Break Indices
Msika womwe mtengo wake umasinthasintha pakati pa malire apamwamba ndi apansi, ndi kuphulika kwadzidzidzi kwapamwamba kapena kwapansi kuti apange malire atsopano. Sinthani malinga ndi kufuna kwanu posankha kuphulika kwa nthawi zilizonse 100 kapena 200 zakugunda malire (pafupifupi).
Multi Step Indices
Ma index awa nthawi zambiri amakwera kapena kutsika ndi masitepe a 0.1, koma nthawi zina amatha kukwera kapena kutsika ndi masitepe a 0.2, 0.25, 0.3, kapena 0.5.
Onani Synthetic Indices zathu
Chinthu | Kukula kwa contract | Ndalama yoyambira | Kukula kochepera | Malire a Vol | Spread yocheperako | Spread yolingana mu % | Leverage yaikulu kwambiri yogwiritsidwa ntchito | Margin yofunika (%) | Swap yayitali (pts) | Swap yochepa (pts) | Maola a malonda (gmt) |
|---|---|---|---|---|---|---|---|---|---|---|---|
AUD Basket | 100 | USD | 0.01 | 10 | 0.161 | 0.03% | 1:1000 | 0.10% | -3.00 | -1.00 | Mon 00:00 - Fri 20:55 GMT |
Boom 100 Index | 1 | USD | 0.1 | 160 | 7.375 | 0.01% | 1:3000 | 0.03% | -5.00 | -5.00 | Lamlungu 00:00 - Loweruka 24:00 GMT |
Boom 1000 Index | 1 | USD | 0.2 | 250 | 1.7245 | 0.01% | 1:600 | 0.17% | -36.00 | -36.00 | Lamlungu 00:00 - Loweruka 24:00 GMT |
Boom 150 Index | 1 | USD | 0.5 | 1300 | 0.1705 | 0.00% | 1:2000 | 0.05% | -5.00 | -5.00 | Lam 00:00 - Low 24:00 GMT |
Boom 200 Index | 1 | USD | 0.1 | 130 | 7.615 | 0.01% | 1:2000 | 0.05% | -6.00 | -6.00 | Lamlungu 00:00 - Loweruka 24:00 GMT |
Boom 300 Index | 1 | USD | 0.5 | 1000 | 0.5 | 0.12% | 1:100 | 1.00% | -36.00 | -36.00 | Lamlungu 00:00 - Loweruka 24:00 GMT |
Boom 50 Index | 1 | USD | 0.1 | 200 | 1.2719 | 0.00% | 1:4000 | 0.03% | -3.50 | -3.50 | Lamlungu 00:00 - Loweruka 24:00 GMT |
Boom 500 Index | 1 | USD | 0.2 | 500 | 0.535 | 0.01% | 1:400 | 0.25% | -23.00 | -23.00 | Lamlungu 00:00 - Loweruka 24:00 GMT |
Boom 600 Index | 1 | USD | 0.2 | 470 | 0.774 | 0.01% | 1:400 | 0.25% | -36.00 | -36.00 | Lam 00:00 - Lov 24:00 GMT |
Boom 900 Index | 1 | USD | 0.2 | 340 | 0.968 | 0.01% | 1:400 | 0.25% | -32.00 | -32.00 | Lamlungu 00:00 - Loweruka 24:00 GMT |
Zambirizi ndi zochokera ku deta yaposachedwa kwambiri ya malonda ndipo zitha kusiyana ndi mikhalidwe ya malonda ya lero. Zopezeka zitha kusiyana malinga ndi mkhalidwe wa malonda.
Mmene mungachitire malonda a Synthetic Indices pa Deriv
ma CFD
Ganizirani mmene mitengo ya Synthetic Indices ikusinthira mwa kugwiritsa ntchito leverage yaikulu ndi zida zapamwamba za technical indicators.

Options
Nenani zomwe mukuganiza zidzachitika pa msika wa Synthetic Indices popanda kutaya zambiri kuposa amene mwayika poyamba.







